Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Akorinto 11:23-26

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

23 Pakuti zimene ndinalandira kwa Ambuye ndi zomwe ndinakupatsani. Ambuye Yesu, usiku umene anaperekedwa uja, anatenga buledi. 24 Atayamika ndi kumunyema ananena kuti, "Ili ndi thupi langa lomwe laperekedwa kwa inu; muzichita zimenezi pokumbukira Ine." 25 Chimodzimodzi, atatha kudya, anatenga chikho, nati, "Chikho ichi ndi pangano latsopano la magazi anga; imwani nthawi zonse pokumbukira Ine." 26 Pakuti nthawi zonse pamene mudya bulediyu ndikumwa chikhochi, mukulalikira imfa ya Ambuye mpaka Iye adzabweranso.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    23 Pakuti ine nidalandila kwa Ambuye yajha mayaluzo nidakupelekelani, kuti usiku ujha Ambuye Yesu, yapo wadachochedwa wadatenga bumunda, 24 wadamuyamika Mnungu, wadaubandhula, wadakamba, "Ili nithupi langa, ilo lachochedwa ndande yanu. Chitani chimwechi kwa kunikumbukila." 25 Chimwechijha, pambuyo pakudya wadatenga chiko niwakamba, "Chikho ichi ni chipangano cha chipano cha Mnungu, chichimikizidwa kwa mwazi wanga. Chitani chimwechi kila yapo mkumwa, kwa kunikumbukila."

    26 Pakuti kila yapo simujhidya bumunda ili ni kumwa mchikho ichi, muuzila wina Ambuye adafa ndande yanu mbaka yapo siwajhe.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.