11 Kodi ndani mwa anthu angadziwe maganizo a munthu wina, kupatula mzimu wa munthuyo wokhala mʼkati mwake? Chimodzimodzinso palibe amene adziwa maganizo a Mulungu kupatula Mzimu wa Mulunguyo. 12 Mzimu amene tinalandira ife si wa dziko lapansi koma Mzimu wochokera kwa Mulungu wotipatsa ife mwaulere. 13 Izi ndi zimene timayankhula osati mʼmawu wophunzitsidwa ndi nzeru za munthu koma mʼmawu wophunzitsidwa ndi Mzimu, kufotokozera zoonadi zauzimu mʼmawu auzimu.
Publicidade
1 Akorinto 2:11-13
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
11 Palibe mundhu uyo wajhiwa maganizo ya mundhu mwina. Chimchijha mzimu wokha ulimkati nde ujhiwa maganizo ya mundhu mmeneyo, chimwecho ndeumo ili ata kwa Mnungu, Mzimu wokha wa Mnungu nde ujhiwa maganizo ya Mnungu. 12 Sitidalandile Mzimu wa jhiko nambho ife talandila Mzimu ujha wachokela kwa Mnungu, chimwecho sitijhiwe vonjhe ivo Mnungu watipacha ife.
13 Chimwecho sitikamba kwa mau ayaluza ali ni hekima, nambho mau wa yaluza Mzimu wa Mnungu, tikambilila vindhu va Uzimu kwa onjhe ali ni Mzimu wa Mnungu.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.