Pular para o conteúdo
Publicidade

2 Akorinto 9:6,8,10,11

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

Kupereka Mowolowamanja

6 Takumbukirani mawu awa: Amene adzala pangʼono, adzakololanso pangʼono, ndipo amene adzala zochuluka, adzakololanso zochuluka. 8 Ndipo Mulungu akhoza kukudalitsani kwambiri, kuti inuyo nthawi zonse mukhale ndi zinthu zokukwanirani, ndiponso ndi zina zochuluka kuti muthandize pa ntchito zonse zabwino.

10 Tsono Mulungu amene amapereka mbewu kwa wofesa, ndiponso chakudya kuti adye, adzaperekanso mbewu mʼnkhokwe zanu ndi kuzichulukitsa. Iye adzachulukitsanso zipatso za chilungamo chanu. 11 Adzakulemeretsani pa zonse kuti mukhale owolowamanja pa nthawi zonse. Ndipo kuwolowamanja kwanu kudzera mwa ife, kudzakhala kuthokoza kwa Mulungu.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    6 Zindikilani mau yaya, uyo wavyala pang’ono wakolola pang’ono, uyo wavyala zambili wakolola zambili. 8 Mnungu wakhoza kukupachani anyiimwe kupitilila yayo muyafuna, dala mkhale ni kila chindhu icho muchifuna siku zonjhe, dala mpunde kuthangatila kwa kila njhito iyo ili yabwino.

    10 Mnungu uyo wampacha mlimi mbeu ndande yovyala niuyo wampacha chakudya, siwakupacheni mbeu izo muzifuna, siwazichite zimele, zikule ni kukupachani vokolola vambili va ubwino wanu. 11 Iye siwakuchiteni kupata kwa kila kandhu, dala kwa ubwino wanu wandhu amuyamike Mnungu, kupitila ife.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.