29 Tsopano, Ambuye taonani kuti atiopseza, tithandizeni ife atumiki anu, kuti tiyankhule mawu anu molimba mtima. 30 Tambasulani dzanja lanu kuchiritsa anthu ndipo kuti, zizindikiro zodabwitsa zichitike mʼdzina la mtumiki wanu woyera Yesu."
Publicidade
Machitidwe a Atumwi 4:29,30
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
29 Chipano Ambuye, onani kuofya kwao. Mutikhozeche ife mbowa wanu kuyakamba mau yanu popande mandha yaliyonjhe. 30 Langizani mbhavu zanu kuti mwaalamiche wandhu, mchite vodabwicha kwa jhina la Mwana wanu Yesu Woyela."
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.