Pular para o conteúdo
Publicidade

Machitidwe a Atumwi 4:29-31

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

29 Tsopano, Ambuye taonani kuti atiopseza, tithandizeni ife atumiki anu, kuti tiyankhule mawu anu molimba mtima. 30 Tambasulani dzanja lanu kuchiritsa anthu ndipo kuti, zizindikiro zodabwitsa zichitike mʼdzina la mtumiki wanu woyera Yesu."

31 Iwo atatha kupemphera, malo amene anasonkhanapo anagwedezeka. Ndipo iwo onse anadzazidwa ndi Mzimu Woyera ndipo anayankhula Mawu a Mulungu molimba mtima.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    29 Chipano Ambuye, onani kuofya kwao. Mutikhozeche ife mbowa wanu kuyakamba mau yanu popande mandha yaliyonjhe. 30 Langizani mbhavu zanu kuti mwaalamiche wandhu, mchite vodabwicha kwa jhina la Mwana wanu Yesu Woyela."

    31 Yapo adangomaliza kupembhela, pamalo pajha adakomanilana padatingizika. Wandhu onjhe adajhazidwa ni Mzimu Woyela ni kukamba mau la Mnungu popande mandha.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.