Pular para o conteúdo
Publicidade

Akolose 3:5-9

5 Choncho, iphani zilakolako za dziko lapansi mwa inu, monga: dama, zodetsa, kulakalaka zosayenera, kukhumba zoyipa ndi umbombo, pakuti umbombo ndiko kupembedza mafano. 6 Chifukwa cha zimenezi, mkwiyo wa Mulungu ukubwera pa ana osamvera. 7 Inunso kale munkachita zomwezi, mʼmoyo wanu wakale uja. 8 Koma tsopano mukuyenera kuzichotsa zinthu zonsezi monga: mkwiyo, ukali, dumbo, chipongwe ndi mawu onyansa. 9 Musanamizane wina ndi mnzake, popeza munavula munthu wakale pamodzi ndi zochita zake

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Colossenses
Ver todos os capítulos de Colossenses