Pular para o conteúdo
Publicidade

Aefeso 1:3-6

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

Madalitso Auzimu mwa Khristu

3 Tiyamike Mulungu, Atate a Ambuye athu Yesu Khristu, amene anatipatsa madalitso onse a uzimu kumwamba mwa Khristu. 4 Dziko lapansi lisanalengedwe, Mulungu anatisankhiratu mwa Khristu kuti tikhale oyera mtima ndi wopanda cholakwa pamaso pake. Mwa chikondi chake, 5 Iye anakonzeratu kuti ife titengedwe ngati ana mwa Yesu Khristu, molingana ndi kukonda kwake ndi chifuniro chake. 6 Anachita zimenezi kuti tiziyamika ulemerero wa chisomo chake, umene watipatsa kwaulere mwa Khristu amene amamukonda.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    3 Watamandidwe Mnungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Kilisito! Ndande ya kulunjana ni Kilisito watipacha mwawi wambili wa mzimu kuchoka kumwamba. 4 Jhiko likali losaumbwidwe, Mnungu wadatisangha tikhale wao pakulunjana ni Kilisito, dala tikhale wandhu yawo tasanghidwa ni Mnungu, yawo tilibe chimo pachogolo pake. Ndande ya chikondi chake, 5 jhiko likali losaumbidwe Mnungu kutisangha, tikhale wana wake kupitila Yesu Kilisito nde umo wadakondela ni chifuno chake mwene.

    6 Chimwecho, timtamande Mnungu kwa ulemelelo wa ubwino wake uwo watipacha ife kwakupitila mwana wake wa payokha.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.