Pular para o conteúdo
Publicidade

Aefeso 4:1-3

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

Umodzi Mʼthupi la Khristu

1 Ine monga wamʼndende chifukwa chotumikira Ambuye, ndikukulimbikitsani kuti mukhale moyo woyenera mayitanidwe amene munalandira. 2 Mukhale odzichepetsa kwathunthu ndi ofatsa; mukhale oleza mtima, ololerana wina ndi mnzake mwachikondi. 3 Muyesetse kusunga umodzi wa Mzimu; umodzi umene umatimangirira pamodzi mu mtendere.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    1 Ndiipo ine nili omangidwa ndande ya kwatumikila Ambuye, nikupembhani kupunda mukhale ngati umo Mnungu wakutanilani. 2 Mkhale ojhichicha ni apole, mlimbilane mitima mwachinawene kwa mwachinawene kwa chikondi. 3 Limbichani umojhi wa Mzimu wa Mnungu, ni mkhale kwa mtendele pakati panu.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.