10 "Amene akhulupirika pa zinthu zochepa akhoza kukhulupirikanso pa zinthu zambiri, ndipo amene sakhulupirika pa zinthu zochepa adzakhala wosakhulupirika pa zinthu zambiri. 11 Ndipo ngati simunakhale okhulupirika pogwiritsa ntchito chuma cha dziko lapansi, ndani amene adzakusungitsani chuma chenicheni?
Publicidade
Luka 16:10,11
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
10 Waliyonjhe uyo wakhoza kukhulupika pavindhu vochepa kupunda, siwakhoze kukhulupilika kwa vindhu vavikulu. Waliyonjhe uyo siwakhulupika pa vindhu vochepa siwakhulipilika pa vindhu vavikulu. 11 Chimwecho, ngati siudakhale okhulupilika pakutumila chuma chapajhiko lapanjhi, yani uyo siwakukhulupilileni kukupachani chuma cha uzimu?
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.