Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 3:8,12,13

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

8 Onetsani zipatso zakutembenuka mtima, ndipo musamanene mwa inu nokha kuti, ‘Tili nalo kholo lathu Abrahamu,’ pakuti ndikuwuzani kuti kuchokera ku miyala iyi, Mulungu akhoza kumuwutsira Abrahamuyo ana.

12 Amisonkho nawonso anabwera kudzabatizidwa. Iwo anafunsa kuti, "Aphunzitsi, ife tichite chiyani?"

13 Iye anawawuza kuti, "Musalandire moposa zimene muyenera."

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    8 Ngati mujha mtengo wa vipacho ufunika kubala, nianyiimwe mlangize kwa vichito kuti mwasiya machimo yanu. Osati muyambe kujhikambila mmitima mwanu kuti, ‘Tilinawo ambuyathu Ibilahimu.’ Nikukambilani kuti Mnungu wakhoza kuichita miyala iyi kukhala mbadwa wa Ibulahimu.

    12 Wolandila malipilo naonjho adafika kuti abatizidwe, adamfunjha, "Oyaluza, ni ife ifunika tichite chiyani?" 13 Iye wadaakambila, "Msadalandila malipilo yayakulu kupitilila yayo mwakambilidwa."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.