Atumwi Khumi ndi Awiri
12 Tsiku lina, masiku amenewo, Yesu anapita ku phiri kukapemphera ndipo anakhala usiku wonse akupemphera kwa Mulungu. 13 Kutacha, anayitana ophunzira ake ndipo anasankha khumi ndi awiri a iwo amene anawayika kukhala atumwi:

12 Siku limojhi Yesu wadapita kuphili kupembhela, wadachezela kumweko usiku wonjhe uku ni waapembha a Mnungu. 13 Umawa wake wadaatana oyaluzidwa wake, pakati pa oyaluzidwa ameneo wadaasangha atumwi khumi ni awili, ni wadatana atumwi.
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.