6 Iye anayankha kuti, "Yesaya ananena zoona pamene ananenera za inu achiphamaso; monga kunalembedwa kuti:
"Anthu awa amandilemekeza Ine ndi milomo yawo,
koma mitima yawo ili kutali ndi Ine.
7 Amandilambira Ine kwachabe;
ndi kuphunzitsa malamulo ndi malangizo a anthu.
8 Mwasiya malamulo a Mulungu ndipo mwagwiritsitsa miyambo ya anthu."