23 "Tsoka kwa inu, aphunzitsi amalamulo ndi Afarisi, achiphamaso! Mumapereka chakhumi cha timbewu tonunkhira ndi cha timbewu tokometsera chakudya. Koma mwasiya zofunikira kwambiri za mʼmalamulo monga chilungamo, chifundo ndi kukhulupirika. Muyenera kuchita zomalizirazi komanso osasiya zoyambazo. 24 Atsogoleri akhungu inu! Mumachotsa kantchentche mu chakumwa chanu koma mumameza ngamira.
Publicidade
Mateyu 23:23,24
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
23 "Simvutike anyiimwe oyaluza athauko ni Afalisayo! Anyiimwe ni agunghuli pakuti mwalipicha wandhu zaka ya matelele yayo yanunghila bwino, manjano ni chitowe nambho musiya kuyagwila mayaluzo yayakulu ya thauko, ngati kuvomelezeka ni lisungu ni chikulupi. Nambho mfunika mvichite ivi ni msidavisiya vijha vina. 24 Anyiimwe achogoleli osapenya! Mchocha njhenjhe mmajhi, nambho mmeza ngamila!"
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.