Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateyu 4:5-7

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

5 Pamenepo mdierekezi anapita naye ku mzinda woyera namuyimiritsa pamwamba penipeni pa Nyumba ya Mulungu. 6 Ndipo anati, "Ngati ndinu Mwana wa Mulungu, dziponyeni nokha pansi. Pakuti kwalembedwa:

" ‘Adzalamulira angelo ake za iwe,

ndipo adzakunyamula ndi manja awo

kuti phazi lako lisagunde pa mwala.’ "

7 Yesu anamuyankha kuti, "Kwalembedwanso: ‘Musamuyese Yehova Mulungu wanu.’ "

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    5 Ndiipo Woyesa wadamtenga Yesu mbaka ku Yelusalemu mujhi woyela. Wadamkweza mbaka pamwamba kupunda pa chindupa la nyumba ya Mnungu. 6 Wadamkambila, "Ngati iwe ni Mwana wa Mnungu jhitaye panjhi. Pakuti yalembedwa,

    ‘Mnungu siwakutumile atumiki wake akumwamba

    saakutenge mmanja mwao

    kuti siudajhikhuwala mwendo wako pa mwala.’"

    7 Yesu wadayangha, "Chinchijha yalembedwa, ‘Usadamuyesa Ambuye Mnungu wako.’"

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.