Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateyu 6:1-4

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

Zopereka Zachifundo

1 "Samalani kuti musachite ntchito zanu zolungama pamaso pa anthu kuti akuoneni. Popeza ngati mutero simudzalandira mphotho yochokera kwa Atate anu akumwamba.

2 "Pamene mupereka zachifundo, musachite modzionetsera monga amachita achiphamaso mʼmasunagoge ndi pa misewu kuti atamidwe ndi anthu. Zoonadi, Ine ndikuwuzani kuti iwowo alandiriratu mphotho yawo yonse. 3 Koma pamene mupereka zachifundo, dzanja lanu lamanzere lisadziwe chimene dzanja lanu lamanja likuchita, 4 kotero kuti kupereka kwanu kukhale mwachinsinsi. Ndipo Atate anu amene amaona zochitika mwachinsinsi, adzakupatsani mphotho.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    1 Yesu wadaendekela kukamba, "Mkhale maso msadachita vindhu vabwino pamaso pa wandhu kuti akuoneni. Ngati mchita chimwecho, Atate wanu ali kumwamba saakupachani chikho chalichonjhe."

    2 "Ndiipo yapo umpacha osauka chindhu chilichonjhe usadauzila kwa wandhu. Usadachita ngati agunghuli umo achitila mnyumba yo komanilana Ayahudi ni mnjila kuti wandhu watamande. Zene nikukambilani achameneo atholandila chikho chao chonjhe. 3 Nambho iwe yapo umthangatila osauka chita chimwecho ata mbwenji wako wa pafupi siwadajhiwa. 4 Chindhu chimenecho sichikhale chisisi kwako, Atate wako yao apenya icho wachichita kwa chisisi siakupache chikho."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.