Pular para o conteúdo
Publicidade

Aroma 8:31-34

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

31 Nanga tsono tidzanena chiyani pa izi? Ngati Mulungu ali mbali yathu, adzatitsutsa ife ndani? 32 Iye amene sanatimane Mwana wake wa Iye yekha, koma anamupereka chifukwa cha ife tonse. Iye adzalekeranjinso pamodzi naye kutipatsa ife zinthu zonse mwaulere? 33 Ndani amene adzabweretsa mlandu kutsutsa amene Mulungu anawasankha? Ndi Mulungu amene amalungamitsa. 34 Ndani amene angatipeze ife olakwa? Palibe. Khristu Yesu amene anafa, kuposera pamenepo, amene anaukitsidwa ndi moyo, amene ali kudzanja lamanja la Mulungu ndiye amene akutipempherera.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    31 Kuchokana ni yameneyo, sitikambe chiyani? Ngati Mnungu wali pamojhi ni ife, yani wakoza kutichucha? 32 Mnungu siwadamchekeleze ata Mwana wake wa yokha, ila wadamchocha ndande ya ife wonjhe, ngati wadachita chimwecho, bwanji, siwatipacha mwawi wonjhe? 33 Niyani siwapache mlandu wandhu asanghidwa ni Mnungu? Mnungu mwene wachochela kulakwa kwao! 34 Niyani uyo siwalamule kwa kwalanga? Palibe! Pakuti Kilisito nde uyo wadamwalila, ni wadahyuka ni wakhala kumalo ya ulamulilo kwa Mnungu iye watipembhela.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.