15 Tangoganizirani, mʼbale kapena mlongo amene ali ndi usiwa, ndipo alibe chakudya cha tsiku ndi tsiku. 16 Ngati mmodzi wa inu amuwuza kuti, "Pita ndi mtendere, ukafundidwe ndipo ukakhute," koma osamupatsa zimene akuzisowa, phindu lake nʼchiyani pamenepa?
Publicidade