Publicidade

Ser de confiança

Por Bíblia Online

A confiabilidade é uma marca do caráter cristão. A Bíblia exalta aqueles que são fiéis em suas palavras, compromissos e na missão que Deus lhes confiou.

Fidelidade como vocação

Ser de confiança é refletir o caráter de Deus, que é fiel em todas as suas promessas. A fidelidade se prova nas pequenas e grandes coisas.

Pakuti mawu a Yehova ndi olungama ndi owona;

Iye ndi wokhulupirika pa zonse zimene amachita.

Wantchito Wokhulupirika ndi Wosakhulupirika

"Kodi wantchito wokhulupirika ndi wanzeru amene ambuye ake anamuyika kukhala woyangʼanira antchito a mʼnyumba kuti awapatse chakudya chawo pa nthawi yake ndani?

Anthu onse adzada inu chifukwa cha Ine, koma iye amene apirira mpaka kumapeto, adzapulumuka.

Integridade e verdade

O cristão confiável fala a verdade, cumpre suas promessas e persevera até o fim, mesmo quando o caminho é difícil.

Mʼmalo mwake, poyankhula choonadi mwachikondi, tidzakula mu zinthu zonse ndi kukhala thupi la Khristu, amene ndi Mutu, omwe ndi mpingo. Mwa Iye thupi lonse lalumikizidwa ndi kugwirana pamodzi ndi mitsempha yothandizira. Likukula ndi kudzilimbitsa lokha mwachikondi, pomwe chiwalo chilichonse chikugwira ntchito yake.

Musachite mantha ndi zimene muti musauke nazo posachedwapa. Ndithu, Satana adzayika ena a inu mʼndende pofuna kukuyesani, ndipo mudzazunzika kwa masiku khumi. Khalani okhulupirika ngakhale zitafika pa imfa, ndipo Ine ndidzakupatsani chipewa cha ulemerero wamoyo.

Seja o primeiro
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-07-05_12-11-46-