Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Akorinto 12:4-7,22

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

4 Pali mphatso zosiyanasiyana, koma Mzimu yemweyo. 5 Pali mautumiki osiyanasiyana koma Ambuye yemweyo. 6 Pali magwiridwe antchito osiyanasiyana, koma Mulungu yemweyo amagwira ntchito monsemo mwa anthu onse.

7 Tsono Mzimu amapereka mphatso kwa aliyense kuti ipindulire onse.

22 Mʼmalo mwake, ziwalo zathupi zimene zimaoneka ngati zofowoka ndizo zili zofunikira kwambiri,

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    4 Pali mbhaso zosianasiana za Mzimu wa Mnungu, nambho zonjhe zichoka kwa Mzimu ni mweyujha mmojhi. 5 Tena pali mitundu yosiana yotumikila Ambuye, yonjhe ichoka kwa iye yujha. 6 Pali mitundu yosianasiana yochita njhito, nambho Mnungu ni mmojhi, iye ndeuyo watikhozecha kuchita njhito zonjhe. 7 Nambho, mbhaso za muuzimu apachidwa wandhu osiyanasiyana dala za thangatile wandhu wina.

    22 Nambho pamalo pake, vijha viwalo va thupi ivovioneka vofooka ndeivo vifunika kupunda,

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.