Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Coríntios 7

Ukwati

1 Tsopano pa zinthu zomwe munandilembera nʼkwabwino kuti munthu asakwatire. 2 Koma chifukwa choti chigololo chawanda, mwamuna aliyense akhale naye mkazi wakewake ndipo mkazi aliyense akhale naye mwamuna wakewake.

Veja também