Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Akorinto 7:21-24

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

21 Kodi munali kapolo pamene Mulungu anakuyitanani? Musavutike nazo zimenezi. Koma ngati mutapeza mwayi woti mulandire ufulu, ugwiritseni ntchito mwayiwo. 22 Pakuti amene anali kapolo pamene amayitanidwa ndi Ambuye, ndi mfulu wa Ambuye; chimodzimodzinso amene anali mfulu pamene anayitanidwa, ndi kapolo wa Khristu. 23 Munagulidwa ndi mtengowapatali, choncho musakhalenso akapolo a anthu. 24 Abale, aliyense angokhala pamaso pa Mulungu monga momwe analili pamene Mulungu anamuyitana.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    21 Bwanji udatanidwa uli kapolo? Usadaona kuipa, ngati ukaona ufulu tumila malo ulinayo chipano, kusiyana ni nyengo ina yaliyonjhe. 22 Kwa kapolo watanidwa ni Ambuye iye wakhala mundhu wa ufulu, chimwecho watanidwa wali mundhu wa ufulu iye wakhala kapolo wa Kilisito. 23 Mnungu wakughulani kwa mtengo waukulu, kuti msadakhala kapolo a wandhu. 24 Abale wanga kilammojhi wakhale ni pachogolo pa Mnungu ngati mujha wadali yapo wadatanidwa.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.