Pular para o conteúdo
Publicidade

1 MBIRI 16

34 Yamikani Yehova, pakuti Iye ndi wabwino;

chikondi chake chikhala mpaka muyaya.

35 Fuwulani kuti, "Tipulumutseni, Inu Mulungu wa chipulumutso chathu,

mutisonkhanitse ndipo mutipulumutse kwa anthu a mitundu ina,

kuti tiyamike dzina lanu loyera,

kuti tikutamandeni."

36 Atamandike Yehova Mulungu wa Israeli,

kuyambira muyaya mpaka muyaya.

Ndipo anthu onse anati, "Ameni" ndipo "Tikutamandani Yehova."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também