Pular para o conteúdo
Publicidade

1 MAFUMU 1

11 Pamenepo Natani anafunsa Batiseba, amayi ake a Solomoni, kuti, "Kodi simunamve kuti Adoniya, mwana wa Hagiti, walowa ufumu popanda Davide mbuye wathu kudziwa? 12 Tsopano ine ndikulangizeni inu mmene mungapulumutsire moyo wanu ndi moyo wa mwana wanu Solomoni. 13 Pitani msanga kwa Mfumu Davide ndipo mukanene kuti, Mbuye wanga mfumu, kodi simunalumbire kwa ine mdzakazi wanu kuti, Ndithu mwana wako Solomoni ndiye adzakhale mfumu mʼmalo mwanga, ndipo adzakhala pa mpando wanga waufumu?Nanga nʼchifukwa chiyani Adoniya walowa ufumu?

Veja também