Makwangwala Adyetsa Eliya
1 Ndipo mneneri Eliya wa ku Tisibe ku Giliyadi, anati kwa Ahabu, "Pali Yehova wamoyo, Mulungu wa Israeli, amene ndimamutumikira, sipadzakhala mame kapena mvula zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditanena."

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.