Pular para o conteúdo
Publicidade

1 MAFUMU 3

26 Mayi amene mwana wake anali moyo anagwidwa ndi chisoni chifukwa cha mwana wakeyo ndipo anawuza mfumu kuti, "Chonde mbuye wanga, mupatseni mnzangayu mwana wamoyoyu! Musamuphe!"

Koma winayo anati, "Ayi, asandipatse ine kapena iwe. Muduleni pakati!"

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também