37 Yehova amene anandilanditsa mʼkamwa mwa mkango ndi chimbalangondo adzandilanditsa mʼmanja mwa Mfilisiti uyu."
Sauli anati kwa Davide, "Pita, ndipo Yehova akhale nawe."