11 Ndipo Bokosi la Chipangano la Yehova linalandidwa, ndiponso ana awiri Eli, Hofini ndi Finehasi anaphedwa.
17 Iye anayankha kuti, "Aisraeli athawa pamaso pa Afilisti. Anthu ambirimbiri aphedwa. Ana anunso Hofini ndi Finehasi aphedwa. Bokosi la Mulungu nalonso lalandidwa."
22 Ananena momwemo kuti, "Ulemerero wachoka mu Israeli, pakuti Bokosi la Mulungu lalandidwa."