Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Timoteyo 2:1-4

Malangizo Achipembedzo

1 Tsono choyamba ndikukupemphani kuti mupempherere anthu onse. Mapemphero anu akhale opemba, opempha, opempherera ena ndi oyamika. 2 Mupempherere mafumu ndi onse aulamuliro, kuti tikhale moyo wamtendere ndi bata, woopa Mulungu ndi oyera mtima. 3 Izi ndi zabwino ndipo zimakondweretsa Mulungu Mpulumutsi wathu, 4 amene amafuna kuti anthu onse apulumutsidwe ndipo kuti adziwe choonadi.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.