Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Timóteo 5

Malangizo kwa Amayi Amasiye, Akulu Ampingo ndi Akapolo

1 Usadzudzule munthu wachikulire mokalipa, koma umuchenjeze ngati abambo ako. Achinyamata uwatenge ngati abale ako. 2 Amayi achikulire uwatenge ngati amayi ako ndipo amayi achitsikana uwatenge ngati alongo ako, nʼkuyera mtima konse.

Veja também