Pular para o conteúdo
Publicidade

1 TIMOTEYO 5

17 Akulu ampingo amene amayangʼanira bwino zochitika za mu mpingo, ndi oyenera ulemu wowirikiza, makamaka amene ntchito yawo ndi kulalikira ndi kuphunzitsa. 18 Pakuti Mawu a Mulungu amati, "Musamange ngʼombe pakamwa pamene ikupuntha tirigu," ndi "Wantchito ngoyenera kulandira malipiro ake."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também