6 Nʼchifukwa chake nthawi zonse timalimba mtima, ndipo timadziwa kuti pamene tikukhala mʼthupi, ndiye kuti tili kutali ndi Ambuye. 7 Ife timakhala mwachikhulupiriro, osati mwa zooneka ndi maso. 8 Inde, ife tikulimba mtima, ndipo tikanakonda kulekana nalo thupi lathu ndi kukhala ndi Ambuye. 9 Choncho timayesetsa kukondweretsa Ambuye, ngakhale tikhale mʼthupi, kapena tichokemo.
Publicidade
2 Akorinto 5:6-9
TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
Em outras traduções
- NTNYBL2025 Nyanja
6 Tili nganganga siku zonjhe. Tijhiwa kuti kukhala moyo pathupi ili ni kukhala patali ni Ambuye. 7 Pakuti tikhala kwa chikhulupi, asati kwa yajha tiyaona. 8 Nambho tili nganganga ni tikhumbila kulisiya thupi ili kuti tikhale pamojhi ni Ambuye. 9 Chimwecho chindhu chachikulu kupunda ni kumkwadilicha, ikhale tikhala pano pajhiko kapina kumeneko kumwamba.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.