9 Atawoloka, Eliya anati kwa Elisa, "Ndifotokozere, ndikuchitire chiyani ndisanachotsedwe pamaso pako?"
Elisa anayankha kuti, "Ndikupemphani kuti mundipatse magawo awiri a mphamvu za mzimu wanu wa uneneri."