23 Mwamuna wakeyo anafunsa kuti, "Chifukwa chiyani ukupita kwa iyeyo lero? Lero si tsiku la Chikondwerero cha Mwezi Watsopano kapena tsiku la Sabata."
Mayiyo anayankha kuti, "Zonse zili bwino."