Publicidade

2 Reis 6

16 Mneneri anamuyankha kuti, "Usachite mantha. Amene ali mbali yathu ndi ambiri kupambana amene ali mbali yawo."

17 Ndipo Elisa anapemphera kuti, "Inu Yehova tsekulani maso ake kuti aone." Pamenepo Yehova anatsekula maso a mtumikiyo, ndipo anayangʼana naona kuti phiri lonse linali lodzaza ndi akavalo ndi magaleta a moto atazungulira Elisa.

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-28_14-13-17-