Pular para o conteúdo
Publicidade

2 Timóteo 3

Zoopsa za Mʼmasiku Otsiriza

1 Koma dziwa izi: Mʼmasiku otsiriza kudzafika nthawi zoopsa kwambiri. 2 Anthu adzakhala odzikonda, okonda ndalama, odzitama, onyada, achipongwe, osamvera makolo awo, osayamika, wopanda chiyero. 3 Adzakhala wopanda chikondi, osakhululuka, osinjirira, osadziletsa, ankhanza, osakonda zabwino,

Veja também

2 Timóteo
Ver todos os capítulos de 2 Timóteo