Pular para o conteúdo
Publicidade

AMOSI 7

14 Amosi anayankha Amaziya kuti, "Ine sindine mneneri kapena mwana wa mneneri; koma ndine woweta ziweto, ndiponso mlimi wa nkhuyu. 15 Koma Yehova ananditenga ndikuweta nkhosa ndipo anati, Pita ukanenere kwa anthu anga Aisraeli.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também