11 "Nthawi ikubwera," Ambuye Yehova akunena kuti,
"Ndidzagwetsa njala mʼdziko lonse;
osati njala ya chakudya kapena ludzu la madzi,
koma njala yofuna kumva mawu a Yehova.
11 "Nthawi ikubwera," Ambuye Yehova akunena kuti,
"Ndidzagwetsa njala mʼdziko lonse;
osati njala ya chakudya kapena ludzu la madzi,
koma njala yofuna kumva mawu a Yehova.