7 "Onani akubwera ndi mitambo,"
ndipo "Aliyense adzamuona,
ndi amene anamubaya omwe."
Ndipo anthu a mitundu yonse ya pa dziko lapansi "adzalira chingʼangʼadza chifukwa cha Iye."
Zidzakhaladi momwemo, Ameni.