Pular para o conteúdo
Publicidade

Apocalipse 11

Lipenga Lachisanu ndi Chiwiri

15 Mngelo wachisanu ndi chiwiri anawomba lipenga lake, ndipo kumwamba kunamveka mawu ofuwula amene anati,

"Ufumu wa dziko lapansi uli

mʼmanja mwa Ambuye athu ndi Khristu wake uja,

ndipo adzalamulira mpaka muyaya."

Veja também