4 Komabe ndili ndi chotsutsana nawe: Wataya chikondi chako chapoyamba. 5 Kumbukirani kuti munagwa kuchokera patali. Lapa ndikuchita zinthu zimene unkachita poyamba. Ngati sulapa ndidzabwera ndikukuchotsera choyikapo nyale chako pamalo pake.
Publicidade