Pular para o conteúdo
Publicidade

CHIVUMBULUTSO 5

Buku la Mwana Wankhosa

1 Kenaka ndinaona buku mʼdzanja la wokhala pa mpando waufumu uja. Bukulo linali lolembedwa mbali zonse ndipo linali lomatidwa ndi zomatira zisanu ndi ziwiri. 2 Ndipo ndinaona mngelo wamphamvu akulengeza ndi mawu okweza kuti, "Ndani ali woyenera kumatula zomatira ndi kufutukula bukuli?"

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também