Pular para o conteúdo
Publicidade

MACHITIDWE A ATUMWI 13

2 Iwo pamene ankapembedza Ambuye ndi kusala kudya, Mzimu Woyera anati, "Mundipatulire Barnaba ndi Saulo kuti akagwire ntchito imene ndinawayitanira." 3 Ndipo atasala kudya ndi kupemphera anasanjika manja awo pa iwo nawatumiza.

Ku Kupro

4 Barnaba ndi Saulo motumidwa ndi Mzimu Woyera, anapita ku Selukeya ndipo kuchokera kumeneko anakwera sitima ya pamadzi kupita ku Kupro.

Veja também