Pular para o conteúdo
Publicidade

MACHITIDWE A ATUMWI 18

Ku Korinto

1 Zitatha izi, Paulo anachoka ku Atene ndipo anapita ku Korinto. 2 Kumeneko anakumana ndi Myuda wina dzina lake Akula, nzika ya ku Ponto amene anali atangofika kumene kuchokera ku Italiya pamodzi ndi mkazi wake Prisila, chifukwa Klaudiyo analamula Ayuda onse kuti achoke ku Roma. Paulo anapita kukawaona. 3 Popeza Paulo anali mʼmisiri wosoka matenti monga iwo, iye anakhala nawo namagwirira ntchito pamodzi.

Veja também