11 Iye ndi
" ‘Mwala umene amisiri omanga nyumba anawukana,
umenewo wasanduka mwala wa pa ngodya!’
12 Chipulumutso sichipezeka mwa wina aliyense; pakuti palibe dzina lina pansi pa thambo limene lapatsidwa kwa anthu limene tiyenera kupulumutsidwa nalo."