Pular para o conteúdo
Publicidade

MACHITIDWE A ATUMWI 6

9 Panauka mtsutso kuchokera kwa anthu a ku Kurene ndi a ku Alekisandriya komanso a ku dera la Silisiya ndi Asiya, otchedwa a Sunagoge ya Mfulu. Anthu amenewa anayamba kutsutsana ndi Stefano.

11 Iwo ananyengerera anthu ena mwamseri kuti anene kuti, "Ife tinamva Stefano akuchitira chipongwe Mose ndiponso Mulungu."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também