Pular para o conteúdo
Publicidade

MACHITIDWE A ATUMWI 7

42 Koma Mulungu anawafulatira, nawapereka kuti apembedze zolengedwa zakumwamba. Zimenezi zikugwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼbuku la aneneri kuti,

" Kodi pa zaka makumi anayi zimene munakhala mʼchipululu muja

munkandibweretsera nsembe ndi zopereka, inu nyumba ya Israeli?

43 Ayi, inu mwanyamula tenti ya Moloki

ndi nyenyezi ya mulungu wanu Refani,

mafano amene munapanga kuti muziwapembedza.

Chifukwa chake, Ine ndidzakutumizani kutali, kupitirira dziko la Babuloni.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também