5 Saulo anafunsa kuti, "Ndinu yani Ambuye?"
Ambuye anayankha kuti, "Ndine Yesu amene iwe ukumuzunza." 6 "Tsopano dzuka, lowa mu mzindamo, ndipo udzawuzidwa zoyenera kuchita."