Publicidade

Efésios 6

Ana ndi Makolo Awo

1 Inu ana, mverani makolo anu mwa Ambuye, pakuti zimenezi ndi zoyenera. 2 "Lemekeza abambo ndi amayi ako." Limeneli ndi lamulo loyamba lokhala ndi lonjezo. 3 Ngati ulemekeza abambo ako ndi amayi ako, "zinthu zidzakuyendera bwino ndipo udzasangalala ndi moyo wautali pa dziko lapansi."

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-29_22-07-56-