Pular para o conteúdo
Publicidade

EKSODO 11

Mliri wa Imfa ya Ana Oyamba Kubadwa

1 Tsopano Yehova anati kwa Mose, "Ine ndidzalanga Farao pamodzi ndi Aigupto onse ndi mliri umodzi wotsiriza. Zikadzachitika izi iye adzakulolani kuti mutuluke mʼdziko lino. Ndithu pamene azidzakutulutsani adzachita ngati akukuyingitsani.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também