Pular para o conteúdo
Publicidade

EKSODO 12

24 "Muzimvera malamulo amenewa kwa muyaya, inu ndi zidzukulu zanu. 25 Mukakalowa mʼdziko limene Yehova adzakupatseni monga analonjeza, mukasunge mwambo umenewu. 26 Ndipo ana anu akakakufunsani kuti, Mwambo umenewu ukutanthauza chiyani?27 Inu mukawawuze kuti, Ndi nsembe ya Paska ya Yehova, popeza pamene ankakantha nyumba za Aigupto anasiya nyumba zathu.’ " Kenaka anthu anawerama napembedza.

Veja também